Yobu 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amauza Mulungu woona kuti, ‘Chokani kwa ife!+Sitikufuna kudziwa njira zanu.+ Salimo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+