Yobu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso amene amauza Mulungu woona kuti: ‘Tichokereni!+Kodi Wamphamvuyonse angatichite chiyani?’ Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+ Salimo 73:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anena kuti: “Mulungu angadziwe bwanji?+Kodi Wam’mwambamwamba akudziwa zimenezi?”+
11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+