Salimo 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikhululukireni machimo anga,+Ndipo fafanizani zolakwa zanga zonse.+ Salimo 73:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anena kuti: “Mulungu angadziwe bwanji?+Kodi Wam’mwambamwamba akudziwa zimenezi?”+