Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Monga mmene kum’mawa kwatalikirana ndi kumadzulo,+Momwemonso, watiikira kutali zolakwa zathu.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+ Yeremiya 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+
17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+
17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+