Salimo 113:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuyambira kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera,+Dzina la Yehova liyenera kutamandidwa.+