Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:11 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, ptsa. 19-20
11 Mumtima mwake amanena kuti: “Mulungu waiwala zoipa zimene ndimachita.+ Iye wayangʼana kumbali. Sakuona chilichonse.”+