Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:11 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, ptsa. 19-20
11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+