Salimo 79:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+ Yesaya 64:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Palibe amene akutamanda dzina lanu.+ Palibe amene akutekeseka kuti akufunefuneni ndi kukugwirani mwamphamvu, pakuti mwatibisira nkhope yanu+ ndipo mwatichititsa kuti tisungunuke+ ndi mphamvu ya zolakwa zathu.
6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+
7 Palibe amene akutamanda dzina lanu.+ Palibe amene akutekeseka kuti akufunefuneni ndi kukugwirani mwamphamvu, pakuti mwatibisira nkhope yanu+ ndipo mwatichititsa kuti tisungunuke+ ndi mphamvu ya zolakwa zathu.