Salimo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+ Hoseya 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onsewo akutentha ngati ng’anjo yamoto, ndipo akuwononga oweruza awo. Mafumu awo onse agwa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akundiitana.+
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+
7 Onsewo akutentha ngati ng’anjo yamoto, ndipo akuwononga oweruza awo. Mafumu awo onse agwa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akundiitana.+