Yesaya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo sanabwerere kwa amene akuwamenya+ ndipo sanafunefune Yehova wa makamu,+ Ezekieli 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala+ ndi kuima pamalo ogumuka a mpandawo+ kuti ateteze dzikolo n’cholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense. Danieli 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Masoka onse amene analembedwa m’chilamulo cha Mose+ atigwera,+ ndipo ife sitinakhazike pansi mtima wanu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kusiya zolakwa zathu+ ndi kusonyeza kuti tikumvetsa kuti ndinu wokhulupirika.+
30 “‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala+ ndi kuima pamalo ogumuka a mpandawo+ kuti ateteze dzikolo n’cholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.
13 Masoka onse amene analembedwa m’chilamulo cha Mose+ atigwera,+ ndipo ife sitinakhazike pansi mtima wanu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kusiya zolakwa zathu+ ndi kusonyeza kuti tikumvetsa kuti ndinu wokhulupirika.+