Yeremiya 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu+ amene akunyalanyazani,+ ndi pa mafuko amene sakuitana padzina lanu.+ Pakuti iwo adya Yakobo.+ Amudya ndipo akupitirizabe kumuwononga.+ Malo ake okhalamo awasandutsa bwinja.+ Amosi 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani izi amuna inu, inu amene mukufuna kumeza munthu wosauka+ ndiponso amene mukufuna kufafaniza anthu ofatsa padziko lapansi.+ Mika 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwadya mnofu wa anthu anga+ ndipo mwasenda khungu lawo. Mwaswa mafupa awo kukhala zidutswazidutswa. Mwawaphwanyaphwanya ngati mafupa ndi mnofu zimene zili mumphika wakukamwa kwakukulu komanso ngati nyama imene ili mumphika.+
25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu+ amene akunyalanyazani,+ ndi pa mafuko amene sakuitana padzina lanu.+ Pakuti iwo adya Yakobo.+ Amudya ndipo akupitirizabe kumuwononga.+ Malo ake okhalamo awasandutsa bwinja.+
4 “Tamverani izi amuna inu, inu amene mukufuna kumeza munthu wosauka+ ndiponso amene mukufuna kufafaniza anthu ofatsa padziko lapansi.+
3 Mwadya mnofu wa anthu anga+ ndipo mwasenda khungu lawo. Mwaswa mafupa awo kukhala zidutswazidutswa. Mwawaphwanyaphwanya ngati mafupa ndi mnofu zimene zili mumphika wakukamwa kwakukulu komanso ngati nyama imene ili mumphika.+