Yesaya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+
22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+