Yeremiya 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mahatchi ake akumveka kupuma mwawefuwefu ali ku Dani.+ Dziko lonse layamba kugwedezeka chifukwa cha phokoso la kulira kwa mahatchi ake amphongo.+ Adani akubwera kudzawononga dziko ndi zonse zokhala mmenemo, mzinda ndi onse okhala mmenemo.” Maliro 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munaitana+ anthu kuchokera kumalo onse ozungulira, kumene akukhala monga alendo.Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe wothawa kapena wopulumuka.+Ana onse athanzi amene ndinabereka ndi kuwalera, mdani wanga anawapha.+
16 Mahatchi ake akumveka kupuma mwawefuwefu ali ku Dani.+ Dziko lonse layamba kugwedezeka chifukwa cha phokoso la kulira kwa mahatchi ake amphongo.+ Adani akubwera kudzawononga dziko ndi zonse zokhala mmenemo, mzinda ndi onse okhala mmenemo.”
22 Munaitana+ anthu kuchokera kumalo onse ozungulira, kumene akukhala monga alendo.Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe wothawa kapena wopulumuka.+Ana onse athanzi amene ndinabereka ndi kuwalera, mdani wanga anawapha.+