Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 46:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.

  • Amosi 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndinaona Yehova ataima pamwamba pa guwa lansembe,+ ndipo anati: “Menya mutu wa chipilala kuti maziko ake agwedezeke ndipo udulenso mitu ya zipilala zonse.+ Ndiyeno otsala mwa anthuwo ndidzawapha ndi lupanga. Aliyense wa iwo amene adzathawa ndidzamuphabe, aliyense wa iwo amene adzathawa sadzapulumuka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena