Yesaya 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera m’dzenje,+ ndipo aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha. Pakuti zotsekera madzi akumwamba zidzatseguka+ ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.+ Yesaya 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera pamahatchi n’kuthawa!”+ N’chifukwa chake mudzathawe. Munanenanso kuti: “Tidzakwera pamahatchi othamanga kwambiri!”+ N’chifukwa chake anthu okuthamangitsani adzakhale othamanga kwambiri.+ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera m’dzenje,+ ndipo aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha. Pakuti zotsekera madzi akumwamba zidzatseguka+ ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.+
16 Ndipo munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera pamahatchi n’kuthawa!”+ N’chifukwa chake mudzathawe. Munanenanso kuti: “Tidzakwera pamahatchi othamanga kwambiri!”+ N’chifukwa chake anthu okuthamangitsani adzakhale othamanga kwambiri.+
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+