Deuteronomo 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzawonjezera masoka awo,+Mivi yanga ndidzaithera pa iwo.+ 1 Mafumu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu amene anatsala anathawira kumzinda wa Afeki,+ ndipo khoma linagwera amuna 27,000 amene anatsala.+ Beni-hadadi anathawa+ ndipo pomalizira pake anafika mumzindawo n’kulowa m’chipinda chamkati.+
30 Anthu amene anatsala anathawira kumzinda wa Afeki,+ ndipo khoma linagwera amuna 27,000 amene anatsala.+ Beni-hadadi anathawa+ ndipo pomalizira pake anafika mumzindawo n’kulowa m’chipinda chamkati.+