Yesaya 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera m’dzenje,+ ndipo aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha. Pakuti zotsekera madzi akumwamba zidzatseguka+ ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.+ Yeremiya 48:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+ “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova. Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+ Amosi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akabisala pamwamba pa phiri la Karimeli, ndidzawafufuza mosamala ndi kuwatenga,+ ndipo akathawa pamaso panga ndi kubisala pansi pa nyanja,+ ndidzalamula njoka pansi pa nyanja pomwepo kuti iwalume.
18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera m’dzenje,+ ndipo aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha. Pakuti zotsekera madzi akumwamba zidzatseguka+ ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.+
44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+ “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova.
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
3 Akabisala pamwamba pa phiri la Karimeli, ndidzawafufuza mosamala ndi kuwatenga,+ ndipo akathawa pamaso panga ndi kubisala pansi pa nyanja,+ ndidzalamula njoka pansi pa nyanja pomwepo kuti iwalume.