Yobu 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kulibe mdima wandiweyaniWoti amene akuchita zopweteka ena abisaleko.+ Salimo 139:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndingapite kuti kuthawa mzimu wanu,+Ndipo ndingapite kuti kuthawa nkhope yanu?+ Yeremiya 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kodi munthu aliyense angabisale m’malo obisika ine osamuona?”+ watero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene chingabisike kwa ine?”+ watero Yehova.
24 “Kodi munthu aliyense angabisale m’malo obisika ine osamuona?”+ watero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene chingabisike kwa ine?”+ watero Yehova.