Yeremiya 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.
24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.