Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+
11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+