Genesis 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Motero Mulungu anapanga mlengalenga. Anapanganso cholekanitsa madzi, kuti ena akhale pansi pa mlengalenga, ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Genesis 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya.
7 Motero Mulungu anapanga mlengalenga. Anapanganso cholekanitsa madzi, kuti ena akhale pansi pa mlengalenga, ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.
2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya.