Genesis 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Galamukani!,3/2014, tsa. 6
7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.