Genesis 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Motero Mulungu anapanga mlengalenga. Anapanganso cholekanitsa madzi, kuti ena akhale pansi pa mlengalenga, ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Galamukani!,3/2014, tsa. 6
7 Motero Mulungu anapanga mlengalenga. Anapanganso cholekanitsa madzi, kuti ena akhale pansi pa mlengalenga, ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.