Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+ Miyambo 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 pamene analimbitsa mitambo yakumwamba,+ pamene anachititsa kuti akasupe a madzi akuya akhale olimba,+
11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+
28 pamene analimbitsa mitambo yakumwamba,+ pamene anachititsa kuti akasupe a madzi akuya akhale olimba,+