Genesis 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma nkhungu+ inali kukwera m’mwamba kuchokera padziko lapansi, ndipo inali kunyowetsa nthaka yonse.+ Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+ Genesis 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya. Salimo 104:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munalikuta ndi madzi ngati mwalikuta ndi nsalu.+Madziwo anakwera kupitirira mapiri.+
6 Koma nkhungu+ inali kukwera m’mwamba kuchokera padziko lapansi, ndipo inali kunyowetsa nthaka yonse.+
11 M’chaka cha 600 cha moyo wa Nowa, m’mwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli akasupe onse amadzi akuya* anaphulika ndipo zotsekera madzi akumwamba zinatseguka.+
2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya.