Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Zomwe zidzachitike n’zakuti, wothawa lupanga la Hazaeli,+ adzaphedwa ndi Yehu,+ ndipo wothawa lupanga la Yehu, adzaphedwa ndi Elisa.+

  • 1 Mafumu 20:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Anthu amene anatsala anathawira kumzinda wa Afeki,+ ndipo khoma linagwera amuna 27,000 amene anatsala.+ Beni-hadadi anathawa+ ndipo pomalizira pake anafika mumzindawo n’kulowa m’chipinda chamkati.+

  • Amosi 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+

  • Amosi 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena