2 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+
24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+