1 Mafumu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zomwe zidzachitike n’zakuti, wothawa lupanga la Hazaeli,+ adzaphedwa ndi Yehu,+ ndipo wothawa lupanga la Yehu, adzaphedwa ndi Elisa.+ Miyambo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+ Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+ Miyambo 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zilango anazikhazikitsira anthu onyoza,+ ndipo zikwapu anazisungira msana wa anthu opusa.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
17 Zomwe zidzachitike n’zakuti, wothawa lupanga la Hazaeli,+ adzaphedwa ndi Yehu,+ ndipo wothawa lupanga la Yehu, adzaphedwa ndi Elisa.+
12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+
25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+