Yesaya 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano musakhale anthu onyoza+ chifukwa zingwe zanu zingakhale zolimba, pakuti ndamva kuchokera kwa Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ kuti dziko lonse laweruzidwa kuti liwonongedwe.+
22 Tsopano musakhale anthu onyoza+ chifukwa zingwe zanu zingakhale zolimba, pakuti ndamva kuchokera kwa Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ kuti dziko lonse laweruzidwa kuti liwonongedwe.+