Yesaya 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano pewani kunyoza+Kuti zingwe zanu asapitirize kuzimanga kwambiri,Chifukwa ndamva kuchokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Kuti waganiza zoti awononge dziko lonseli.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:22 Yesaya 1, ptsa. 295-296, 300-301 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, tsa. 23
22 Tsopano pewani kunyoza+Kuti zingwe zanu asapitirize kuzimanga kwambiri,Chifukwa ndamva kuchokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Kuti waganiza zoti awononge dziko lonseli.*+