Yesaya 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano musakhale anthu onyoza+ chifukwa zingwe zanu zingakhale zolimba, pakuti ndamva kuchokera kwa Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ kuti dziko lonse laweruzidwa kuti liwonongedwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:22 Yesaya 1, ptsa. 295-296, 300-301 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, tsa. 23
22 Tsopano musakhale anthu onyoza+ chifukwa zingwe zanu zingakhale zolimba, pakuti ndamva kuchokera kwa Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ kuti dziko lonse laweruzidwa kuti liwonongedwe.+