Yesaya 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse m’dziko n’kulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga dzikolo,+ n’kubalalitsa anthu okhalamo.+
24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse m’dziko n’kulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga dzikolo,+ n’kubalalitsa anthu okhalamo.+