Miyambo 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Onyoza,+ iye amawanyoza,+ koma ofatsa amawakomera mtima.+ Miyambo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+ Machitidwe 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+ 2 Petulo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+
12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+
41 ‘Inu onyoza zimene ine ndikuchita, mudzaona zimene ndikuchitazo ndi kudabwa nazo. Kenako mudzazimiririka, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pang’ono zimene ndidzachite m’masiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+
3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+