Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+Koma wodzikuza samuyandikira.+ Miyambo 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zilango anazikhazikitsira anthu onyoza,+ ndipo zikwapu anazisungira msana wa anthu opusa.+