Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa Abimeleki ndi kunyeketsa nzika za Sekemu ndi anthu a m’nyumba ya Milo,+ komanso moto+ utuluke mwa nzika za Sekemu ndi anthu a m’nyumba ya Milo ndi kunyeketsa Abimeleki.”+

  • Oweruza 9:57
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+

  • 2 Mafumu 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto+ utsike kumwamba n’kunyeketsa iweyo ndi asilikali ako 50.” Ndipo moto unatsikadi kumwamba n’kunyeketsa mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.+

  • Machitidwe 8:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma Petulo anamuuza kuti: “Siliva wakoyo awonongeke nawe limodzi, chifukwa ukuganiza kuti mphatso yaulere ya Mulungu ungaipeze ndi ndalama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena