Oweruza 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ ndi kulankhula nawo mofuula kuti: “Ndimvereni, inu nzika za Sekemu, ndipo Mulungu akumvereni:
7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ ndi kulankhula nawo mofuula kuti: “Ndimvereni, inu nzika za Sekemu, ndipo Mulungu akumvereni: