Oweruza 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ nʼkulankhula mofuula kuti: “Ndimvereni, inu atsogoleri a ku Sekemu, ndipo mukatero Mulungu akumverani.
7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ nʼkulankhula mofuula kuti: “Ndimvereni, inu atsogoleri a ku Sekemu, ndipo mukatero Mulungu akumverani.