Miyambo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+ Miyambo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+ Hoseya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+
12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+
15 Mtsogoleri woipa wolamulira anthu onyozeka ali ngati mkango wobangula ndiponso chimbalangondo chimene chikubwera kudzakuluma.+
8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+