Yesaya 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu nyama zonse zakutchire, inu nyama zonse za m’nkhalango, bwerani mudzadye.+ Yeremiya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+
9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+