2 Mafumu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri. Ezekieli 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+
2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri.
37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+