Deuteronomo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+ Yeremiya 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ ndipo sadzawalira maliro+ kapena kuikidwa m’manda+ koma adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Iwo adzafa ndi lupanga ndiponso njala yaikulu.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.’+ Hoseya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ngakhale alere ana awo, ine ndidzawaphera anawo moti sadzakula n’kukhala amuna.+ Tsoka kwa iwo ndikadzawachokera!+
18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+
4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ ndipo sadzawalira maliro+ kapena kuikidwa m’manda+ koma adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Iwo adzafa ndi lupanga ndiponso njala yaikulu.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.’+
12 Pakuti ngakhale alere ana awo, ine ndidzawaphera anawo moti sadzakula n’kukhala amuna.+ Tsoka kwa iwo ndikadzawachokera!+