Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 34:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amenewa ndidzawapereka m’manja mwa adani awo ndi m’manja mwa onse ofuna moyo wawo.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka m’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.+

  • Ezekieli 39:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Koma kwa iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Uza mbalame zamitundumitundu ndi zilombo zonse zakutchire+ kuti: “Sonkhanani mubwere kuno. Sonkhanani pamodzi kuzungulira nsembe yanga imene ndikukuperekerani. Imeneyi ndi nsembe yaikulu m’mapiri a ku Isiraeli.+ Mukabwera mudzadya nyama ndi kumwa magazi.+

  • Chivumbulutso 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena