Chivumbulutso 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame zonse zouluka chapafupi mumlengalenga kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni kuphwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 284-285
17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame zonse zouluka chapafupi mumlengalenga kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni kuphwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,+