Yeremiya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+ Zefaniya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.
9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+
7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.