Deuteronomo 28:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+ Deuteronomo 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+ Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+
32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+
25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+
7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+