2 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechi, makolo athu anaphedwa ndi lupanga+ ndipo ana athu aamuna ndi aakazi ndiponso akazi athu anapita ku ukapolo.+ Yoweli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mwagulitsa ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu+ kwa ana a Agiriki,+ ndi cholinga choti muwachotse ndi kuwapititsa kutali ndi dziko lawo,+
9 Pa chifukwa chimenechi, makolo athu anaphedwa ndi lupanga+ ndipo ana athu aamuna ndi aakazi ndiponso akazi athu anapita ku ukapolo.+
6 mwagulitsa ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu+ kwa ana a Agiriki,+ ndi cholinga choti muwachotse ndi kuwapititsa kutali ndi dziko lawo,+