Genesis 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai,+ Yavani,+ Tubala,+ Meseke+ ndi Tirasi.+ Zekariya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yuda ndidzamupinda kuti akhale uta wanga. Efuraimu ndidzamuika pa uta umenewo ngati muvi. Iwe Ziyoni, ine ndidzadzutsa ana ako+ kuti aukire ana a Girisi.+ Ndipo ndidzakusandutsa lupanga la munthu wamphamvu.’+
13 Yuda ndidzamupinda kuti akhale uta wanga. Efuraimu ndidzamuika pa uta umenewo ngati muvi. Iwe Ziyoni, ine ndidzadzutsa ana ako+ kuti aukire ana a Girisi.+ Ndipo ndidzakusandutsa lupanga la munthu wamphamvu.’+