Danieli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+ Yoweli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mwagulitsa ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu+ kwa ana a Agiriki,+ ndi cholinga choti muwachotse ndi kuwapititsa kutali ndi dziko lawo,+
21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+
6 mwagulitsa ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu+ kwa ana a Agiriki,+ ndi cholinga choti muwachotse ndi kuwapititsa kutali ndi dziko lawo,+