Deuteronomo 28:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Yehova adzakubwezerani ku Iguputo pa zombo kudzera njira imene ndinakuuzani kuti, ‘Simudzaionanso.’+ Kumeneko mudzalakalaka kudzigulitsa kwa adani anu kuti mukhale akapolo aamuna ndi aakazi,+ koma sipadzakhala wokugulani.”
68 Yehova adzakubwezerani ku Iguputo pa zombo kudzera njira imene ndinakuuzani kuti, ‘Simudzaionanso.’+ Kumeneko mudzalakalaka kudzigulitsa kwa adani anu kuti mukhale akapolo aamuna ndi aakazi,+ koma sipadzakhala wokugulani.”