Deuteronomo 28:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+ Ezekieli 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.
32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+
13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.